Тексты песен «Langwan Piksy»


1

Langwan Piksy - Bambo Nyimbo

VERSE ONE PIKSY Mmudzi uwu anthu amandikonda kwambiri Amfumu ati ndiime u MP Ati nyimbo za ine ziri amazing Pazokha zitha kukwana kukhala ngati incentive Ku wina u MP no campaign Opikisana nawo akuchita complain...

2

Langwan Piksy - Mpaka Udzipita

Ndikudziwa kuti ndafika mammawa Ndikudziwa zaku bhowa Yeah mtima wako ukuwawa Koma babe ukudziwa za ku bhawa Ndimakupeza wagona Sticheza ngati banja Ine Ndimakhala ndatopa Lonseli ndi vuto langa Mammawa uliwonse...

3

Langwan Piksy - Mthunzi

CHORUS Ndikufuna mthunziwo Sindufuna Nkhunizo Chonde musadule Mtengo wangawo Nthawi zina sitikamba zofunika kukambidwa Sitikankha zofunika kukankhidwa Pena Sitikanda pofunika kukandidwa Dziko linasintha timaopa...

4

Langwan Piksy - Mwezi Uwale

HOOK Mwezi uwale eh Ndikumane ndi dona apa Lija ndi kale eh Mfundo zanga ndiponya apa BRIDGE Kapena ndimenye bibida? Mantha ndiye andidinda Ndikumva ngati ndadzimbidwa Pompano nditha kubibidwq VERSE...

5

Langwan Piksy - Pakati

VERSE ONE Pakati, pa kuwala ndi mdima Pakati, pakutentha ndi kuzizira Pakati, pa chubu ndi mpira Pakati, pa nkhuku ndi dzira Nkakhala ofunda mudzandilavula Sinfuna kulavulidwa Sinfuna kulavulidwa Ndiri ngati munda...

6

Langwan Piksy - Unamata

VERSE ONE Kumata kumata ndi superglue Uli duu Kuutolatola mtima wanga pansi uli mbuu Kumata ndi bostic Mbali zonse kuchta stick 2getha wambawamba osamvetsa yako logic Unali wanga driver So loyal to me sunasamale nkhan...

7

Langwan Piksy - Wako Wako

VERSE 1 Uthenga wa masankha kwa Namazanje Panopa tiri official si za masanje Lero sitisamala za wansanje Tivine ingoma Mkhetekete ndi manganje CHORUS Tinafunitsitsa banja titamanga Koma tinadziwa kufika si ku thamanga...